Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 25:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “Ngati amuna apachibale akukhala moyandikana, ndiyeno mmodzi n’kumwalira asanabereke mwana wamwamuna, mkazi wa womwalirayo asakwatiwe ndi mlendo wochokera m’banja lina. Mlamu wake apite kwa iye ndi kum’tenga kukhala mkazi wake, ndipo achite ukwati wa pachilamu.+

  • Deuteronomo 25:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Mwana woyamba amene mkaziyo angabereke, atenge dzina la mwamuna womwalira uja,+ kuti dzina la m’bale wake lisafafanizike mu Isiraeli.+

  • Rute 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Koma Naomi anati: “Bwererani ana anga. Palibe chifukwa choti tipitire limodzi. Kodi ndingathenso kubereka ana, ndipo kodi anawo angadzakhale amuna anu?+

  • Mateyu 22:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 “Mphunzitsi, Mose anati, ‘Ngati munthu wamwalira wopanda ana, m’bale wake ayenera kukwatira mkazi wamasiyeyo ndi kuberekera m’bale wake uja ana.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena