Genesis 38:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho Yuda anapatukira kwa mkaziyo pambali pa msewu n’kumuuza kuti: “Ndikufuna ndigone nawe.”+ Anatero posadziwa kuti anali mpongozi wake.+ Koma mkaziyo anayankha kuti: “Mundipatsa chiyani kuti mugone nane?”+ Miyambo 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Woyamba kufotokoza mbali yake pa mlandu amaoneka ngati wolondola,+ koma mnzake amabwera n’kumufufuzafufuza.+ 1 Akorinto 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chotero musaweruze+ kalikonse nthawi isanakwane, mpaka Ambuye adzafike.+ Akadzafika adzaunika zinsinsi za mu mdima+ ndi kuonetsa poyera+ zolingalira za m’mitima, ndipo aliyense adzatamandidwa yekha ndi Mulungu.+
16 Choncho Yuda anapatukira kwa mkaziyo pambali pa msewu n’kumuuza kuti: “Ndikufuna ndigone nawe.”+ Anatero posadziwa kuti anali mpongozi wake.+ Koma mkaziyo anayankha kuti: “Mundipatsa chiyani kuti mugone nane?”+
17 Woyamba kufotokoza mbali yake pa mlandu amaoneka ngati wolondola,+ koma mnzake amabwera n’kumufufuzafufuza.+
5 Chotero musaweruze+ kalikonse nthawi isanakwane, mpaka Ambuye adzafike.+ Akadzafika adzaunika zinsinsi za mu mdima+ ndi kuonetsa poyera+ zolingalira za m’mitima, ndipo aliyense adzatamandidwa yekha ndi Mulungu.+