Genesis 31:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Aliyense amene mum’peze ndi milungu yanu aphedwe.+ Pamaso pa abale athuwa, fufuzani milungu yanuyo pa katundu wathu. Mukaipeza muitenge.”+ Koma Yakobo sanadziwe kuti Rakele anali ataba milunguyo.+ Genesis 37:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kenako, iwo anatumiza mkanjo wamizeremizere uja kwa bambo awo. Atafika nawo anati: “Tapeza mkanjo uwu. Chonde, uonetsetseni+ kuti muone ngati uli mkanjo wa mwana wanu kapena ayi.”+ Levitiko 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “‘Musamaweruze mopanda chilungamo. Musamakondere munthu wosauka,+ ndiponso musamakondere munthu wolemera.+ Mnzako uzimuweruza mwachilungamo.
32 Aliyense amene mum’peze ndi milungu yanu aphedwe.+ Pamaso pa abale athuwa, fufuzani milungu yanuyo pa katundu wathu. Mukaipeza muitenge.”+ Koma Yakobo sanadziwe kuti Rakele anali ataba milunguyo.+
32 Kenako, iwo anatumiza mkanjo wamizeremizere uja kwa bambo awo. Atafika nawo anati: “Tapeza mkanjo uwu. Chonde, uonetsetseni+ kuti muone ngati uli mkanjo wa mwana wanu kapena ayi.”+
15 “‘Musamaweruze mopanda chilungamo. Musamakondere munthu wosauka,+ ndiponso musamakondere munthu wolemera.+ Mnzako uzimuweruza mwachilungamo.