Deuteronomo 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Munthu akachita tchimo, mboni imodzi si yokwanira kutsimikizira kuti wachitadi cholakwacho kapena tchimo lililonse.+ Muzitsimikizira nkhaniyo mutamva umboni wapakamwa pa mboni ziwiri kapena zitatu.+ Miyambo 6:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pakuti nsanje ya mwamuna imautsa mkwiyo wake,+ ndipo sadzamva chisoni pa tsiku lobwezera.+ Miyambo 29:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mtsogoleri akamamvera mabodza, onse omutumikira adzakhala oipa.+
15 “Munthu akachita tchimo, mboni imodzi si yokwanira kutsimikizira kuti wachitadi cholakwacho kapena tchimo lililonse.+ Muzitsimikizira nkhaniyo mutamva umboni wapakamwa pa mboni ziwiri kapena zitatu.+