Genesis 41:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inuyo a Farao munatikwiyira kwambiri ife atumiki anu.+ Ineyo ndi mkulu wa ophika mkate munatitsekera m’ndende ya kunyumba kwa mkulu wa asilikali olondera mfumu.+ Miyambo 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mkwiyo wa mfumu umatanthauza amithenga a imfa,+ koma munthu wanzeru ndi amene amauziziritsa.+ Miyambo 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mkwiyo wa mfumu uli ngati kubangula kwa mkango wamphamvu,+ koma kukoma mtima kwake kuli ngati mame pazomera.+
10 Inuyo a Farao munatikwiyira kwambiri ife atumiki anu.+ Ineyo ndi mkulu wa ophika mkate munatitsekera m’ndende ya kunyumba kwa mkulu wa asilikali olondera mfumu.+
12 Mkwiyo wa mfumu uli ngati kubangula kwa mkango wamphamvu,+ koma kukoma mtima kwake kuli ngati mame pazomera.+