Genesis 41:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Pa zaka zonse 7 za chakudya chamwanaalirenji, dzikolo linabereka chakudya chambiri.+ Genesis 47:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Chotero Yosefe anakhazikitsa lamulo limene lilipobe mpaka lero lakuti, Farao azilandira gawo limodzi mwa magawo asanu a zokolola za minda yonse ya mu Iguputo. Koma ansembe, monga gulu lapadera, minda yawo sinakhale ya Farao.+
26 Chotero Yosefe anakhazikitsa lamulo limene lilipobe mpaka lero lakuti, Farao azilandira gawo limodzi mwa magawo asanu a zokolola za minda yonse ya mu Iguputo. Koma ansembe, monga gulu lapadera, minda yawo sinakhale ya Farao.+