Genesis 26:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Zitatero, Isaki anayamba kubzala mbewu m’dzikomo.+ M’chaka chimenechi anakolola zochuluka moti pa mbewu zimene anabzala, anakolola zochuluka kuwirikiza nthawi 100,+ popeza Yehova anali kum’dalitsa.+ Salimo 65:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu mwatembenukira dziko lapansi kuti mulipatse zinthu zochuluka,+Mwalilemeretsa kwambiri.Mtsinje wochokera kwa Mulungu ndi wosefukira ndi madzi.+Munalinganiza zinthu, kuti mbewu zawo zibale.+Umu ndi mmene mumaperekera zinthu padziko lapansi.+
12 Zitatero, Isaki anayamba kubzala mbewu m’dzikomo.+ M’chaka chimenechi anakolola zochuluka moti pa mbewu zimene anabzala, anakolola zochuluka kuwirikiza nthawi 100,+ popeza Yehova anali kum’dalitsa.+
9 Inu mwatembenukira dziko lapansi kuti mulipatse zinthu zochuluka,+Mwalilemeretsa kwambiri.Mtsinje wochokera kwa Mulungu ndi wosefukira ndi madzi.+Munalinganiza zinthu, kuti mbewu zawo zibale.+Umu ndi mmene mumaperekera zinthu padziko lapansi.+