Salimo 104:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Komanso kuti mutuluke vinyo amene amasangalatsa mtima wa munthu.+Amachita zonsezi kuti nkhope ya munthu isalale ndi mafuta,+Komanso kuti apereke chakudya chimene chimakhutiritsa mtima wa munthu.+ Salimo 107:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Anthuwo amafesa mbewu ndi kulima minda ya mpesa,+Kuti akhale ndi zokolola.+
15 Komanso kuti mutuluke vinyo amene amasangalatsa mtima wa munthu.+Amachita zonsezi kuti nkhope ya munthu isalale ndi mafuta,+Komanso kuti apereke chakudya chimene chimakhutiritsa mtima wa munthu.+