Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 11:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Limenelo ndi dziko limene Yehova Mulungu wanu akulisamalira. Nthawi zonse maso+ a Yehova Mulungu wanu amakhala padziko limeneli, kuyambira kuchiyambi kwa chaka mpaka kumapeto.

  • Salimo 104:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Amameretsa msipu kuti nyama zidye,+

      Ndipo amameretsa mbewu kuti anthu agwiritse ntchito.+

      Amachita zimenezi kuti chakudya chituluke m’nthaka,+

  • Salimo 147:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Muimbireni Iye amene amaphimba mapiri ndi mitambo,+

      Amene amakonza mvula kuti igwe padziko lapansi,+

      Amenenso amameretsa udzu wobiriwira m’mapiri.+

  • Machitidwe 14:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Komabe iye sanangokhala wopanda umboni wakuti anachita zabwino.+ Anakupatsani mvula+ kuchokera kumwamba ndi nyengo zimene zokolola zanu zimakhala zambiri. Anadzaza mitima yanu ndi chakudya komanso chimwemwe.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena