Yobu 28:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Padziko lapansi pamamera chakudya,+Koma pansi pake pasandulizidwa ngati kuti pasakazidwa ndi moto. 1 Akorinto 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chotero wobzala+ kapena wothirira sali kanthu, koma Mulungu amene amakulitsa.+