Genesis 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Mulungu anati: “Dziko lapansi limere udzu, limere zomera zobala mbewu,+ limere mitengo yobala zipatso zokhala ndi mbewu yake, monga mwa mtundu wake.”+ Ndipo zinaterodi. Salimo 104:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Amameretsa msipu kuti nyama zidye,+Ndipo amameretsa mbewu kuti anthu agwiritse ntchito.+Amachita zimenezi kuti chakudya chituluke m’nthaka,+
11 Ndiyeno Mulungu anati: “Dziko lapansi limere udzu, limere zomera zobala mbewu,+ limere mitengo yobala zipatso zokhala ndi mbewu yake, monga mwa mtundu wake.”+ Ndipo zinaterodi.
14 Amameretsa msipu kuti nyama zidye,+Ndipo amameretsa mbewu kuti anthu agwiritse ntchito.+Amachita zimenezi kuti chakudya chituluke m’nthaka,+