Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 1:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Tsopano Mulungu anati: “Taonani, ndakupatsani zomera zonse zobala mbewu zapadziko lonse lapansi, ndi mitengo yonse yobala zipatso za mbewu+ kuti zikhale chakudya chanu.+

  • Genesis 3:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Minga ndi zitsamba zobaya* zidzamera panthaka,+ ndipo udzadya zomera za m’nthaka.

  • Genesis 9:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Nyama yamoyo iliyonse ikhale chakudya chanu.+ Komanso ndikukupatsani zamasamba zonse kuti zikhale chakudya chanu.+

  • Yobu 38:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Kuti inyowetse malo owonongeka ndi mvula yamkuntho ndiponso ouma,

      Komanso kuti imeretse udzu?+

  • Aheberi 6:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Mwachitsanzo, nthaka imamwa madzi a mvula imene imagwera panthakapo kawirikawiri. Kenako imatulutsa zomera zimene zimapindulitsa amene ailima.+ Nthaka imeneyi imalandiranso dalitso kuchokera kwa Mulungu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena