2 Samueli 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ulamuliro wake umakhala ngati kuwala kwa m’mawa pamene dzuwa lawala,+M’mawa wopanda mitambo.Umakhala ngati msipu womera padziko mvula ikakata, dzuwa n’kuwala.’+ Salimo 147:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Muimbireni Iye amene amaphimba mapiri ndi mitambo,+Amene amakonza mvula kuti igwe padziko lapansi,+Amenenso amameretsa udzu wobiriwira m’mapiri.+ Aheberi 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mwachitsanzo, nthaka imamwa madzi a mvula imene imagwera panthakapo kawirikawiri. Kenako imatulutsa zomera zimene zimapindulitsa amene ailima.+ Nthaka imeneyi imalandiranso dalitso kuchokera kwa Mulungu.
4 Ulamuliro wake umakhala ngati kuwala kwa m’mawa pamene dzuwa lawala,+M’mawa wopanda mitambo.Umakhala ngati msipu womera padziko mvula ikakata, dzuwa n’kuwala.’+
8 Muimbireni Iye amene amaphimba mapiri ndi mitambo,+Amene amakonza mvula kuti igwe padziko lapansi,+Amenenso amameretsa udzu wobiriwira m’mapiri.+
7 Mwachitsanzo, nthaka imamwa madzi a mvula imene imagwera panthakapo kawirikawiri. Kenako imatulutsa zomera zimene zimapindulitsa amene ailima.+ Nthaka imeneyi imalandiranso dalitso kuchokera kwa Mulungu.