Genesis 41:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Pa zaka 7 zimenezo, Yosefe anasonkhanitsa chakudya chonse chimene anakolola m’dziko lonse la Iguputo, n’kuchisunga m’mizinda.+ Chakudya chonse chochokera m’minda yonse yozungulira mzinda uliwonse, anachisunga pakati pa mzindawo.+ Miyambo 8:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 kuti ndichititse amene amandikonda kulandira zinthu zamtengo wapatali,+ ndipo ndimadzazitsa nkhokwe zawo.+ Machitidwe 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma Yakobo anamva kuti ku Iguputo kuli chakudya,+ ndipo anatuma makolo athu aja kwa nthawi yoyamba.+
48 Pa zaka 7 zimenezo, Yosefe anasonkhanitsa chakudya chonse chimene anakolola m’dziko lonse la Iguputo, n’kuchisunga m’mizinda.+ Chakudya chonse chochokera m’minda yonse yozungulira mzinda uliwonse, anachisunga pakati pa mzindawo.+
21 kuti ndichititse amene amandikonda kulandira zinthu zamtengo wapatali,+ ndipo ndimadzazitsa nkhokwe zawo.+
12 Koma Yakobo anamva kuti ku Iguputo kuli chakudya,+ ndipo anatuma makolo athu aja kwa nthawi yoyamba.+