Genesis 45:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kumeneko ndizidzakupatsani chakudya. Kwatsala zaka zisanu za njala,+ ndipo sindikufuna kuti inuyo ndi a m’nyumba yanu, ndi zonse zimene muli nazo muvutike ndi njala.”’ Genesis 47:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamenepo anthuwo anayamba kubweretsa ziweto zawo kwa Yosefe. Yosefeyo anali kuwapatsa chakudya mosinthana ndi mahatchi* awo, nkhosa, ng’ombe ndi abulu.+ M’chaka chonsecho, Yosefe anali kuwagawira chakudya mosinthana ndi ziweto zawo.
11 Kumeneko ndizidzakupatsani chakudya. Kwatsala zaka zisanu za njala,+ ndipo sindikufuna kuti inuyo ndi a m’nyumba yanu, ndi zonse zimene muli nazo muvutike ndi njala.”’
17 Pamenepo anthuwo anayamba kubweretsa ziweto zawo kwa Yosefe. Yosefeyo anali kuwapatsa chakudya mosinthana ndi mahatchi* awo, nkhosa, ng’ombe ndi abulu.+ M’chaka chonsecho, Yosefe anali kuwagawira chakudya mosinthana ndi ziweto zawo.