Genesis 37:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iwo anamuonera patali akubwera, ndipo asanafike pafupi anayamba kupangana chiwembu choti amuphe.+ Genesis 37:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Tsopano amuna amalonda achimidiyani+ aja anali kudutsa mumsewu. Pamenepo abale a Yosefe anamutulutsa m’chitsimemo+ n’kumugulitsa kwa Aisimaeliwo. Anamugulitsa ndalama zasiliva 20,+ ndipo iwo anapita naye ku Iguputo. Genesis 50:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 ‘Mukamuuze Yosefe kuti: “Chonde ndikukupempha, ukhululuke+ chiwembu cha abale ako, ndi kuchimwa kwawo pa zoipa zimene anakuchitira.”’+ Ndiye chonde, tikhululukireni ife akapolo a Mulungu wa bambo anu.”+ Atamuuza zimenezi, Yosefe analira kwambiri. Machitidwe 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mitu ya mabanja ija inachitira nsanje+ Yosefe ndi kumugulitsa ku Iguputo.+ Koma Mulungu anali naye,+
28 Tsopano amuna amalonda achimidiyani+ aja anali kudutsa mumsewu. Pamenepo abale a Yosefe anamutulutsa m’chitsimemo+ n’kumugulitsa kwa Aisimaeliwo. Anamugulitsa ndalama zasiliva 20,+ ndipo iwo anapita naye ku Iguputo.
17 ‘Mukamuuze Yosefe kuti: “Chonde ndikukupempha, ukhululuke+ chiwembu cha abale ako, ndi kuchimwa kwawo pa zoipa zimene anakuchitira.”’+ Ndiye chonde, tikhululukireni ife akapolo a Mulungu wa bambo anu.”+ Atamuuza zimenezi, Yosefe analira kwambiri.
9 Mitu ya mabanja ija inachitira nsanje+ Yosefe ndi kumugulitsa ku Iguputo.+ Koma Mulungu anali naye,+