Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 32:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Koma mukapanda kuchita zimenezo, ndithu mudzachimwira Yehova.+ Ndipo mukatero, dziwani kuti tchimo lanu lidzakutsatani.+

  • Miyambo 21:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Aliyense wotseka khutu lake kuti asamve kudandaula kwa munthu wonyozeka,+ nayenso adzaitana koma sadzayankhidwa.+

  • Mateyu 7:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 pakuti chiweruzo chimene mukuweruza nacho ena inunso mudzaweruzidwa nacho.+ Ndipo muyezo umene mukuyezera ena, iwonso adzakuyezerani womwewo.+

  • 1 Timoteyo 5:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Machimo a anthu ena amaonekera poyera,+ ndipo zimenezi zimachititsa kuti aweruzidwe. Koma anthu ena, machimo awo amadzaonekera pambuyo pake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena