Genesis 33:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Esau anathamanga kudzakumana naye,+ ndipo anamukumbatira+ ndi kum’psompsona. Atakumbatirana, onse awiri anagwetsa misozi kwambiri. Genesis 46:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pamenepo Yosefe anakonza galeta lake n’kunyamuka kupita kukakumana ndi Isiraeli bambo ake ku Goseni.+ Atangofika kwa bambo akewo, nthawi yomweyo anawakumbatira n’kulira ndi kugwetsa misozi. Anachita zimenezi mobwerezabwereza.+
4 Esau anathamanga kudzakumana naye,+ ndipo anamukumbatira+ ndi kum’psompsona. Atakumbatirana, onse awiri anagwetsa misozi kwambiri.
29 Pamenepo Yosefe anakonza galeta lake n’kunyamuka kupita kukakumana ndi Isiraeli bambo ake ku Goseni.+ Atangofika kwa bambo akewo, nthawi yomweyo anawakumbatira n’kulira ndi kugwetsa misozi. Anachita zimenezi mobwerezabwereza.+