Genesis 33:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Esau anathamanga kudzakumana naye,+ ndipo anamukumbatira+ ndi kum’psompsona. Atakumbatirana, onse awiri anagwetsa misozi kwambiri. Genesis 45:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yosefe atatero, anakumbatira Benjamini m’bale wake n’kuyamba kulira. Nayenso Benjamini analira atakumbatira m’bale wakeyo.+
4 Esau anathamanga kudzakumana naye,+ ndipo anamukumbatira+ ndi kum’psompsona. Atakumbatirana, onse awiri anagwetsa misozi kwambiri.
14 Yosefe atatero, anakumbatira Benjamini m’bale wake n’kuyamba kulira. Nayenso Benjamini analira atakumbatira m’bale wakeyo.+