Ezekieli 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Iwe mwana wa munthu, Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wauza dziko la Isiraeli, kuti: ‘Mapeto! Mapeto afika kumalekezero anayi a dzikoli.+ Amosi 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno anandifunsa kuti: “Kodi ukuona chiyani+ Amosi?” Ndinayankha kuti: “Ndikuona dengu la zipatso za m’chilimwe.”+ Pamenepo Yehova anandiuza kuti: “Mapeto afika pa anthu anga Aisiraeli.+ Sindidzawamveranso chisoni.+ 1 Petulo 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma mapeto a zinthu zonse ayandikira.+ Choncho khalani oganiza bwino,+ ndipo khalani maso kuti musanyalanyaze kupemphera.+
2 “Iwe mwana wa munthu, Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wauza dziko la Isiraeli, kuti: ‘Mapeto! Mapeto afika kumalekezero anayi a dzikoli.+
2 Ndiyeno anandifunsa kuti: “Kodi ukuona chiyani+ Amosi?” Ndinayankha kuti: “Ndikuona dengu la zipatso za m’chilimwe.”+ Pamenepo Yehova anandiuza kuti: “Mapeto afika pa anthu anga Aisiraeli.+ Sindidzawamveranso chisoni.+
7 Koma mapeto a zinthu zonse ayandikira.+ Choncho khalani oganiza bwino,+ ndipo khalani maso kuti musanyalanyaze kupemphera.+