Maliro 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Akutisakasaka kulikonse kumene tikupita,+ moti palibe amene akuyenda m’mabwalo a mizinda yathu.Mapeto athu ayandikira. Masiku athu akwanira, pakuti mapeto athu afika.+ Ezekieli 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Iwe mwana wa munthu, Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wauza dziko la Isiraeli, kuti: ‘Mapeto! Mapeto afika kumalekezero anayi a dzikoli.+
18 Akutisakasaka kulikonse kumene tikupita,+ moti palibe amene akuyenda m’mabwalo a mizinda yathu.Mapeto athu ayandikira. Masiku athu akwanira, pakuti mapeto athu afika.+
2 “Iwe mwana wa munthu, Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wauza dziko la Isiraeli, kuti: ‘Mapeto! Mapeto afika kumalekezero anayi a dzikoli.+