Ezekieli 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Iwe mwana wa munthu, Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wauza dziko la Isiraeli, kuti: ‘Mapeto! Mapeto afika kumalekezero anayi a dzikoli.+ Ezekieli 12:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chotero uwauze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ndithu Ine ndidzathetsa mwambi umenewu ndipo sadzaunenanso ngati mwambi mu Isiraeli.”’+ Koma uwauze kuti, ‘Masiku ayandikira+ ndipo zonse zotchulidwa m’masomphenya zichitikadi.’ Amosi 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno anandifunsa kuti: “Kodi ukuona chiyani+ Amosi?” Ndinayankha kuti: “Ndikuona dengu la zipatso za m’chilimwe.”+ Pamenepo Yehova anandiuza kuti: “Mapeto afika pa anthu anga Aisiraeli.+ Sindidzawamveranso chisoni.+
2 “Iwe mwana wa munthu, Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wauza dziko la Isiraeli, kuti: ‘Mapeto! Mapeto afika kumalekezero anayi a dzikoli.+
23 Chotero uwauze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ndithu Ine ndidzathetsa mwambi umenewu ndipo sadzaunenanso ngati mwambi mu Isiraeli.”’+ Koma uwauze kuti, ‘Masiku ayandikira+ ndipo zonse zotchulidwa m’masomphenya zichitikadi.’
2 Ndiyeno anandifunsa kuti: “Kodi ukuona chiyani+ Amosi?” Ndinayankha kuti: “Ndikuona dengu la zipatso za m’chilimwe.”+ Pamenepo Yehova anandiuza kuti: “Mapeto afika pa anthu anga Aisiraeli.+ Sindidzawamveranso chisoni.+