Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 25:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Gulu lankhondo la Akasidi+ linayamba kuthamangitsa mfumuyo ndipo linaipeza+ m’chipululu cha Yeriko.+ Pamenepo gulu lonse lankhondo la mfumuyo linabalalika n’kuisiya yokha.

  • Yeremiya 39:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndiyeno Zedekiya mfumu ya Yuda ndi amuna onse ankhondo ataona adaniwo anayamba kuthawira+ kunja kwa mzinda usiku. Iwo analowera njira ya kumunda wa mfumu,+ kukatulukira pachipata chimene chinali pakati pa makoma awiri, n’kupitiriza kuthawa molowera ku Araba.+

  • Maliro 3:52
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 52 Adani anga akundisaka ngati mbalame+ popanda chifukwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena