-
Deuteronomo 33:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
“Dziko lake lipitirize kudalitsidwa ndi Yehova.+
Lidalitsidwe ndi zinthu zabwino kwambiri zakumwamba, mame,+
Ndi madzi akuya a pansi pa nthaka.+
-