Genesis 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mtsinje woyamba dzina lake ndi Pisoni, umene umazungulira dziko lonse la Havila+ kumene kuli golide. Genesis 25:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iwo anakhala m’mahema kuyambira ku Havila+ pafupi ndi Shura+ moyang’anana ndi Iguputo, mpaka ku Asuri. Anakhala pafupi ndi abale awo onse.+
11 Mtsinje woyamba dzina lake ndi Pisoni, umene umazungulira dziko lonse la Havila+ kumene kuli golide.
18 Iwo anakhala m’mahema kuyambira ku Havila+ pafupi ndi Shura+ moyang’anana ndi Iguputo, mpaka ku Asuri. Anakhala pafupi ndi abale awo onse.+