Genesis 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho Sarai anauza Abulamu kuti: “Yehova ananditseka kuti ndisabereke ana.+ Tsopano gonani ndi kapolo wanga. Mwinatu ndingapeze ana kuchokera kwa iye.”+ Chotero Abulamu anamvera mawu a Sarai.+ Genesis 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Abulahamu ndi Sara anali okalamba ndipo anali ndi zaka zambiri.+ Sara anali atasiya kusamba.+ Aroma 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiponso, ngakhale kuti chikhulupiriro chake sichinafooke, anaganizira za thupi lake, limene linali lakufa tsopano,+ popeza anali ndi zaka pafupifupi 100.+ Anaganiziranso zakuti Sara anali wosabereka.+ Aheberi 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mwa chikhulupiriro, Sara+ nayenso analandira mphamvu yokhala ndi pakati* ngakhale kuti anali atapitirira zaka zobereka,+ chifukwa anaona kuti wolonjezayo ndi wokhulupirika.+
2 Choncho Sarai anauza Abulamu kuti: “Yehova ananditseka kuti ndisabereke ana.+ Tsopano gonani ndi kapolo wanga. Mwinatu ndingapeze ana kuchokera kwa iye.”+ Chotero Abulamu anamvera mawu a Sarai.+
19 Ndiponso, ngakhale kuti chikhulupiriro chake sichinafooke, anaganizira za thupi lake, limene linali lakufa tsopano,+ popeza anali ndi zaka pafupifupi 100.+ Anaganiziranso zakuti Sara anali wosabereka.+
11 Mwa chikhulupiriro, Sara+ nayenso analandira mphamvu yokhala ndi pakati* ngakhale kuti anali atapitirira zaka zobereka,+ chifukwa anaona kuti wolonjezayo ndi wokhulupirika.+