18Kenako Yehova anaonekera+ kwa Abulahamu pakati pa mitengo ikuluikulu ya ku Mamure.+ Pa nthawiyi n’kuti Abulahamu atakhala pansi pakhomo la hema wake masana dzuwa likutentha.+
9 Chotero ana ake, Isaki ndi Isimaeli, anamuika iye m’manda. Anamuika m’phanga la Makipela, kumalo a Efuroni mwana wa Zohari Mheti, moyang’anana ndi Mamure.+