Genesis 17:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma za Isimaeli ndamva pempho lako. Iye ndidzamudalitsa ndipo ndidzamupatsa ana ambiri, komanso ndidzachulukitsa kwambiri mbadwa zake.+ Atsogoleri 12 a mafuko adzatuluka mwa iye, ndipo ndidzamupangitsa kukhala mtundu waukulu.+
20 Koma za Isimaeli ndamva pempho lako. Iye ndidzamudalitsa ndipo ndidzamupatsa ana ambiri, komanso ndidzachulukitsa kwambiri mbadwa zake.+ Atsogoleri 12 a mafuko adzatuluka mwa iye, ndipo ndidzamupangitsa kukhala mtundu waukulu.+