Genesis 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako mngelo wa Yehovayo anamuuzanso kuti: “Ndidzachulukitsa kwambiri mbewu yako,+ moti idzakhala yosawerengeka.”+ Genesis 21:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kunena za mwana wa mdzakaziyo,+ nayenso ndidzamupangitsa kukhala mtundu, chifukwa iye ndi mbewu yako.”+ Genesis 25:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Awa ndiwo mayina a ana a Isimaeli, amene kunachokera mabanja awo: Nebayoti,+ mwana woyamba wa Isimaeli, Kedara,+ Adibeele, Mibisamu,+
10 Kenako mngelo wa Yehovayo anamuuzanso kuti: “Ndidzachulukitsa kwambiri mbewu yako,+ moti idzakhala yosawerengeka.”+
13 Kunena za mwana wa mdzakaziyo,+ nayenso ndidzamupangitsa kukhala mtundu, chifukwa iye ndi mbewu yako.”+
13 Awa ndiwo mayina a ana a Isimaeli, amene kunachokera mabanja awo: Nebayoti,+ mwana woyamba wa Isimaeli, Kedara,+ Adibeele, Mibisamu,+