Genesis 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako mngelo wa Yehovayo anamuuzanso kuti: “Ndidzachulukitsa kwambiri mbewu yako,+ moti idzakhala yosawerengeka.”+ Genesis 17:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma za Isimaeli ndamva pempho lako. Iye ndidzamudalitsa ndipo ndidzamupatsa ana ambiri, komanso ndidzachulukitsa kwambiri mbadwa zake.+ Atsogoleri 12 a mafuko adzatuluka mwa iye, ndipo ndidzamupangitsa kukhala mtundu waukulu.+ Genesis 25:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano nayi mbiri ya Isimaeli+ mwana wa Abulahamu, amene Hagara Mwiguputo, kapolo wa Sara anaberekera Abulahamu.+
10 Kenako mngelo wa Yehovayo anamuuzanso kuti: “Ndidzachulukitsa kwambiri mbewu yako,+ moti idzakhala yosawerengeka.”+
20 Koma za Isimaeli ndamva pempho lako. Iye ndidzamudalitsa ndipo ndidzamupatsa ana ambiri, komanso ndidzachulukitsa kwambiri mbadwa zake.+ Atsogoleri 12 a mafuko adzatuluka mwa iye, ndipo ndidzamupangitsa kukhala mtundu waukulu.+
12 Tsopano nayi mbiri ya Isimaeli+ mwana wa Abulahamu, amene Hagara Mwiguputo, kapolo wa Sara anaberekera Abulahamu.+