Aroma 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Chotero malinga ndi zilakolako za m’mitima mwawo, Mulungu anawasiya kuti achite zonyansa,+ kuti matupi awo+ achitidwe chipongwe.+ 2 Petulo 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndipo anthu amenewa, mofanana ndi nyama zopanda nzeru zimene zimabadwira kuti zidzagwidwe ndi kuwonongedwa, amalankhula monyoza za zinthu zimene sakuzidziwa,+ moti adzawonongedwa chifukwa cha njira yawo yachiwonongeko, Yuda 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma anthu amenewa amalankhula monyoza zinthu zonse zimene sakuzidziwa bwinobwino,+ ndipo ali ngati nyama zopanda nzeru. Pochita zinthu zawo zonse zimene amazichita mwachibadwa, amakhala ngati nyama+ ndipo mwa kutero amapitiriza kudziipitsa.+
24 Chotero malinga ndi zilakolako za m’mitima mwawo, Mulungu anawasiya kuti achite zonyansa,+ kuti matupi awo+ achitidwe chipongwe.+
12 Ndipo anthu amenewa, mofanana ndi nyama zopanda nzeru zimene zimabadwira kuti zidzagwidwe ndi kuwonongedwa, amalankhula monyoza za zinthu zimene sakuzidziwa,+ moti adzawonongedwa chifukwa cha njira yawo yachiwonongeko,
10 Koma anthu amenewa amalankhula monyoza zinthu zonse zimene sakuzidziwa bwinobwino,+ ndipo ali ngati nyama zopanda nzeru. Pochita zinthu zawo zonse zimene amazichita mwachibadwa, amakhala ngati nyama+ ndipo mwa kutero amapitiriza kudziipitsa.+