Genesis 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno anati: “Chonde ambuyanga, patukirani kunyumba ya kapolo wanu. Tikusambitseni mapazi ndiponso mukagone,+ kuti mawa mulawirire n’kupitiriza ulendo wanu.”+ Ndiyeno iwo anati: “Ayi, ife tigona m’bwalo la mzinda usiku wa lero.”+ Oweruza 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Atatero anatengera Mlevi uja kunyumba kwake+ ndipo anapatsa abulu ake aja chakudya.+ Ndiyeno anasamba mapazi awo+ n’kuyamba kudya ndi kumwa.
2 Ndiyeno anati: “Chonde ambuyanga, patukirani kunyumba ya kapolo wanu. Tikusambitseni mapazi ndiponso mukagone,+ kuti mawa mulawirire n’kupitiriza ulendo wanu.”+ Ndiyeno iwo anati: “Ayi, ife tigona m’bwalo la mzinda usiku wa lero.”+
21 Atatero anatengera Mlevi uja kunyumba kwake+ ndipo anapatsa abulu ake aja chakudya.+ Ndiyeno anasamba mapazi awo+ n’kuyamba kudya ndi kumwa.