Genesis 30:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Rakele atabereka Yosefe, nthawi yomweyo Yakobo anauza Labani kuti: “Ndiloleni ndizipita kwathu, kudziko lakwathu.+ Genesis 31:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 N’chifukwa chiyani wathawa mwamseri, kundizembera osandiuza? Bwenzi nditatsanzikana nawe mosangalala, nyimbo zikuimbidwa,+ ndiponso maseche ndi azeze akulira.+
25 Rakele atabereka Yosefe, nthawi yomweyo Yakobo anauza Labani kuti: “Ndiloleni ndizipita kwathu, kudziko lakwathu.+
27 N’chifukwa chiyani wathawa mwamseri, kundizembera osandiuza? Bwenzi nditatsanzikana nawe mosangalala, nyimbo zikuimbidwa,+ ndiponso maseche ndi azeze akulira.+