Ekisodo 39:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno anapanga malaya odula manja+ ovala mkati mwa efodi, a nsalu yowomba ndi ulusi wabuluu wokhawokha. Levitiko 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Atatero anaveka Aroni mkanjo+ ndi kum’manga lamba wa pamimba.+ Anamuvekanso malaya odula manja+ komanso efodi,*+ ndi kum’manga kwambiri ndi lamba+ wa efodiyo.
22 Ndiyeno anapanga malaya odula manja+ ovala mkati mwa efodi, a nsalu yowomba ndi ulusi wabuluu wokhawokha.
7 Atatero anaveka Aroni mkanjo+ ndi kum’manga lamba wa pamimba.+ Anamuvekanso malaya odula manja+ komanso efodi,*+ ndi kum’manga kwambiri ndi lamba+ wa efodiyo.