Ekisodo 28:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Ndiyeno upange malaya odula manja ndi ulusi wabuluu wokhawokha, ovala mkati mwa efodi.+ Ekisodo 39:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno anapanga malaya odula manja+ ovala mkati mwa efodi, a nsalu yowomba ndi ulusi wabuluu wokhawokha. Numeri 15:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 ‘Chingwecho chikhale ngati mphonje kwa inu, kuti mukachiyang’ana muzikumbukira malamulo onse+ a Yehova ndi kuwasunga. Muleke kutsatira zilakolako za mitima yanu ndi maso anu,+ chifukwa potsatira zilakolako zimenezo, mukuchita chiwerewere.+ Salimo 119:129 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 129 Zikumbutso zanu n’zodabwitsa.+N’chifukwa chake ine ndimazisunga.+
22 Ndiyeno anapanga malaya odula manja+ ovala mkati mwa efodi, a nsalu yowomba ndi ulusi wabuluu wokhawokha.
39 ‘Chingwecho chikhale ngati mphonje kwa inu, kuti mukachiyang’ana muzikumbukira malamulo onse+ a Yehova ndi kuwasunga. Muleke kutsatira zilakolako za mitima yanu ndi maso anu,+ chifukwa potsatira zilakolako zimenezo, mukuchita chiwerewere.+