1 Mafumu 18:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iwo anapitiriza kuchita ngati aneneri+ mpaka dzuwa linapendeka. Anapitirizabe mpaka nthawi yopereka nsembe yambewu, koma sipanamveke mawu alionse. Palibe anawayankha kapena kuwamvera.+ Salimo 141:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pemphero langa likhale lokonzedwa ngati zofukiza+ pamaso panu,+Mapembedzero anga akhale ngati nsembe yambewu yamadzulo.+
29 Iwo anapitiriza kuchita ngati aneneri+ mpaka dzuwa linapendeka. Anapitirizabe mpaka nthawi yopereka nsembe yambewu, koma sipanamveke mawu alionse. Palibe anawayankha kapena kuwamvera.+
2 Pemphero langa likhale lokonzedwa ngati zofukiza+ pamaso panu,+Mapembedzero anga akhale ngati nsembe yambewu yamadzulo.+