Yesaya 44:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iye akudya phulusa.+ Mtima wake umene wanyengedwa wamusocheretsa.+ Iye sakupulumutsa moyo wake kapena kunena kuti: “Kodi chinthu chimene chili m’dzanja langa lamanjachi si chonyenga?”+ Agalatiya 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngakhale zili choncho, pamene munali osadziwa Mulungu,+ munali akapolo a zinthu zimene mwachilengedwe si milungu.+
20 Iye akudya phulusa.+ Mtima wake umene wanyengedwa wamusocheretsa.+ Iye sakupulumutsa moyo wake kapena kunena kuti: “Kodi chinthu chimene chili m’dzanja langa lamanjachi si chonyenga?”+
8 Ngakhale zili choncho, pamene munali osadziwa Mulungu,+ munali akapolo a zinthu zimene mwachilengedwe si milungu.+