1 Samueli 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsiku lotsatira,+ mzimu woipa wochokera kwa Mulungu unayamba kugwira ntchito pa Sauli,+ moti anayamba kuchita zinthu ngati mneneri+ m’nyumba mwake. Pa nthawiyi, Davide anali kuimba nyimbo+ ngati kale ndipo Sauli anali ndi mkondo m’manja mwake.+ 1 Mafumu 22:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mfumu ya Isiraeli ndi Yehosafati mfumu ya Yuda anali atakhala pabwalo* la pachipata cha Samariya. Aliyense anakhala pampando wake wachifumu atavala zovala zachifumu.+ Pamaso pawo panali aneneri onse ndipo anali kuchita zinthu monga mmene aneneri amachitira.+
10 Tsiku lotsatira,+ mzimu woipa wochokera kwa Mulungu unayamba kugwira ntchito pa Sauli,+ moti anayamba kuchita zinthu ngati mneneri+ m’nyumba mwake. Pa nthawiyi, Davide anali kuimba nyimbo+ ngati kale ndipo Sauli anali ndi mkondo m’manja mwake.+
10 Mfumu ya Isiraeli ndi Yehosafati mfumu ya Yuda anali atakhala pabwalo* la pachipata cha Samariya. Aliyense anakhala pampando wake wachifumu atavala zovala zachifumu.+ Pamaso pawo panali aneneri onse ndipo anali kuchita zinthu monga mmene aneneri amachitira.+