Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 28:43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 43 Aroni ndi ana ake azivala makabudula amenewa polowa m’chihema chokumanako kapena popita kuguwa lansembe kukatumikira pamalo oyera, kuti asapalamule mlandu ndi kufa. Limeneli ndi lamulo kwa iye ndi mbadwa zake mpaka kalekale.+

  • 2 Mbiri 4:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Iye anapanganso mabeseni 10. Anaika mabeseni asanu mbali ya kudzanja lamanja, mabeseni asanu mbali ya kumanzere.+ M’mabeseniwo anali kutsukiramo ndi kutsukuluziramo+ zinthu zokhudzana ndi nsembe yopsereza.+ Ansembe anali kusamba madzi ochokera m’thanki ija.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena