Genesis 30:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Rakele atabereka Yosefe, nthawi yomweyo Yakobo anauza Labani kuti: “Ndiloleni ndizipita kwathu, kudziko lakwathu.+ Machitidwe 7:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “Patapita zaka 40, mngelo anaonekera kwa iye m’malawi a moto pachitsamba chaminga+ m’chipululu, pafupi ndi phiri la Sinai.
25 Rakele atabereka Yosefe, nthawi yomweyo Yakobo anauza Labani kuti: “Ndiloleni ndizipita kwathu, kudziko lakwathu.+
30 “Patapita zaka 40, mngelo anaonekera kwa iye m’malawi a moto pachitsamba chaminga+ m’chipululu, pafupi ndi phiri la Sinai.