Ekisodo 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Farao akakanena kuti, ‘Ndisonyezeni chozizwitsa,’+ iweyo ukauze Aroni kuti, ‘Tenga ndodo yako+ ndi kuiponya patsogolo pa Farao.’ Akakatero, idzasanduka njoka yaikulu.”+
9 “Farao akakanena kuti, ‘Ndisonyezeni chozizwitsa,’+ iweyo ukauze Aroni kuti, ‘Tenga ndodo yako+ ndi kuiponya patsogolo pa Farao.’ Akakatero, idzasanduka njoka yaikulu.”+