Yesaya 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Pempha chizindikiro kwa Yehova Mulungu wako.+ Chikhoza kukhala chozama ngati Manda kapena chachitali ngati malo okwera.” Mateyu 12:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Poyankha iye anawauza kuti: “M’badwo woipa ndi wachigololo+ ukufunitsitsabe chizindikiro. Sudzapatsidwa chizindikiro chilichonse koma chizindikiro cha mneneri Yona chokha.+ Yohane 6:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiyeno iwo anamufunsa kuti: “Ndiye inuyo muchita chizindikiro+ chotani, kuti ife tichione, ndi kukukhulupirirani? Muchita ntchito yotani?
11 “Pempha chizindikiro kwa Yehova Mulungu wako.+ Chikhoza kukhala chozama ngati Manda kapena chachitali ngati malo okwera.”
39 Poyankha iye anawauza kuti: “M’badwo woipa ndi wachigololo+ ukufunitsitsabe chizindikiro. Sudzapatsidwa chizindikiro chilichonse koma chizindikiro cha mneneri Yona chokha.+
30 Ndiyeno iwo anamufunsa kuti: “Ndiye inuyo muchita chizindikiro+ chotani, kuti ife tichione, ndi kukukhulupirirani? Muchita ntchito yotani?