Genesis 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiye nditsikirako kuti ndikaone ngati akuchitadi monga mwa kudandaula kumene ndamva ndiponso ngati zochita zawo zilidi zoipa choncho. Ndikufuna ndidziwe zimenezi.”+ Deuteronomo 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Muzikumbukira njira yonse imene Yehova Mulungu wanu anakuyendetsani m’chipululu zaka 40 zonsezi.+ Iye anakuyendetsani m’chipululu kuti akuphunzitseni kudzichepetsa,+ kukuyesani+ pofuna kudziwa zimene zinali mumtima mwanu,+ kuti aone ngati mukanasunga malamulo ake kapena ayi. Salimo 139:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndifufuzeni, inu Mulungu, ndi kudziwa mtima wanga.+Ndisanthuleni ndi kudziwa malingaliro anga amene akundisowetsa mtendere,+
21 Ndiye nditsikirako kuti ndikaone ngati akuchitadi monga mwa kudandaula kumene ndamva ndiponso ngati zochita zawo zilidi zoipa choncho. Ndikufuna ndidziwe zimenezi.”+
2 Muzikumbukira njira yonse imene Yehova Mulungu wanu anakuyendetsani m’chipululu zaka 40 zonsezi.+ Iye anakuyendetsani m’chipululu kuti akuphunzitseni kudzichepetsa,+ kukuyesani+ pofuna kudziwa zimene zinali mumtima mwanu,+ kuti aone ngati mukanasunga malamulo ake kapena ayi.
23 Ndifufuzeni, inu Mulungu, ndi kudziwa mtima wanga.+Ndisanthuleni ndi kudziwa malingaliro anga amene akundisowetsa mtendere,+