Genesis 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako, Yehova anatsikirako kukaona mzinda ndi nsanja imene ana a anthu anali kumanga.+ Ekisodo 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova anawonjezeranso kuti: “Ndaona nsautso ya anthu anga amene ali ku Iguputo, ndipo ndamva kulira kwawo chifukwa cha amene akuwagwiritsa ntchito mwankhanza. Zoonadi, ndikudziwa bwino zowawa zawo.+ Yoswa 22:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Wamphamvu,+ Mulungu,+ Yehova,+ Wamphamvu, Mulungu, Yehova, iye akudziwa,+ ndipo nayenso Isiraeli adziwa.+ Ngati tachita zimenezi chifukwa chopanduka+ ndiponso chifukwa cha kusakhulupirika pamaso pa Yehova,+ musatisiye amoyo lero. Salimo 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma kuchokera kumwamba, Yehova wayang’ana ana a anthu padziko lapansi,+Kuti aone ngati pali aliyense wozindikira, aliyense amene akufunafuna Yehova.+
7 Yehova anawonjezeranso kuti: “Ndaona nsautso ya anthu anga amene ali ku Iguputo, ndipo ndamva kulira kwawo chifukwa cha amene akuwagwiritsa ntchito mwankhanza. Zoonadi, ndikudziwa bwino zowawa zawo.+
22 “Wamphamvu,+ Mulungu,+ Yehova,+ Wamphamvu, Mulungu, Yehova, iye akudziwa,+ ndipo nayenso Isiraeli adziwa.+ Ngati tachita zimenezi chifukwa chopanduka+ ndiponso chifukwa cha kusakhulupirika pamaso pa Yehova,+ musatisiye amoyo lero.
2 Koma kuchokera kumwamba, Yehova wayang’ana ana a anthu padziko lapansi,+Kuti aone ngati pali aliyense wozindikira, aliyense amene akufunafuna Yehova.+