Levitiko 19:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 “‘Anthu aimvi uziwagwadira,+ munthu wachikulire uzim’patsa ulemu+ ndipo uziopa Mulungu wako.+ Ine ndine Yehova.
32 “‘Anthu aimvi uziwagwadira,+ munthu wachikulire uzim’patsa ulemu+ ndipo uziopa Mulungu wako.+ Ine ndine Yehova.