Ekisodo 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Aroni atangomaliza kulankhula ndi khamu lonse la ana a Isiraeli, iwo anatembenuka ndi kuyang’ana kuchipululu. Ndipo taonani! Ulemerero wa Yehova unaonekera mumtambo.+ Ekisodo 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kwa ana a Isiraeli, ulemerero wa Yehova unali kuoneka ngati moto wolilima+ pamwamba pa phiri.
10 Ndiyeno Aroni atangomaliza kulankhula ndi khamu lonse la ana a Isiraeli, iwo anatembenuka ndi kuyang’ana kuchipululu. Ndipo taonani! Ulemerero wa Yehova unaonekera mumtambo.+