Ekisodo 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova anali kuyenda patsogolo pawo mumtambo woima njo ngati chipilala powatsogolera usana,+ ndipo usiku anali kuwatsogolera m’moto woima njo ngati chipilala kuti uziwaunikira, kuti apitirizebe ulendo usana ndi usiku.+ Numeri 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kora atasonkhanitsa khamu+ lonse lotsutsana nawo pakhomo la chihema chokumanako, ulemerero wa Yehova unaonekera kwa khamu lonselo.+ 1 Mafumu 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa cha mtambowo, ansembewo+ analephera kupitiriza kutumikira,+ popeza ulemerero+ wa Yehova unadzaza nyumba ya Yehovayo.+ Mateyu 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mawu ake adakali m’kamwa, mtambo wowala kwambiri unawaphimba, ndipo panamveka mawu kuchokera mumtambomo akuti: “Uyu ndiye Mwana wanga wokondedwa, amene ndikukondwera naye,+ muzimumvera.”+
21 Yehova anali kuyenda patsogolo pawo mumtambo woima njo ngati chipilala powatsogolera usana,+ ndipo usiku anali kuwatsogolera m’moto woima njo ngati chipilala kuti uziwaunikira, kuti apitirizebe ulendo usana ndi usiku.+
19 Kora atasonkhanitsa khamu+ lonse lotsutsana nawo pakhomo la chihema chokumanako, ulemerero wa Yehova unaonekera kwa khamu lonselo.+
11 Chifukwa cha mtambowo, ansembewo+ analephera kupitiriza kutumikira,+ popeza ulemerero+ wa Yehova unadzaza nyumba ya Yehovayo.+
5 Mawu ake adakali m’kamwa, mtambo wowala kwambiri unawaphimba, ndipo panamveka mawu kuchokera mumtambomo akuti: “Uyu ndiye Mwana wanga wokondedwa, amene ndikukondwera naye,+ muzimumvera.”+