Ekisodo 31:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo inetu ndaika Oholiabu mwana wamwamuna wa Ahisama wa fuko la Dani+ kuti athandize Bezaleli. Komanso ndaika nzeru mumtima wa munthu aliyense waluso, kuti apange zonse zimene ndakulamulazi:+ Ekisodo 35:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Mulungu waika luso lophunzitsa mumtima mwa Bezaleli ndi mwa Oholiabu+ mwana wamwamuna wa Ahisama wa fuko la Dani. Ekisodo 36:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo Mose anaitana Bezaleli, Oholiabu ndi mwamuna aliyense wa mtima wanzeru amene Yehova anaika nzeru mumtima mwake.+ Anaitana aliyense amene anali ndi mtima wofunitsitsa kugwira ntchitoyi.+
6 Ndipo inetu ndaika Oholiabu mwana wamwamuna wa Ahisama wa fuko la Dani+ kuti athandize Bezaleli. Komanso ndaika nzeru mumtima wa munthu aliyense waluso, kuti apange zonse zimene ndakulamulazi:+
34 Mulungu waika luso lophunzitsa mumtima mwa Bezaleli ndi mwa Oholiabu+ mwana wamwamuna wa Ahisama wa fuko la Dani.
2 Pamenepo Mose anaitana Bezaleli, Oholiabu ndi mwamuna aliyense wa mtima wanzeru amene Yehova anaika nzeru mumtima mwake.+ Anaitana aliyense amene anali ndi mtima wofunitsitsa kugwira ntchitoyi.+