Levitiko 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamenepo Mose ndi Aroni analowa m’chihema chokumanako, kenako anatulukamo n’kudalitsa anthuwo.+ Atatero, ulemerero wa Yehova+ unaonekera kwa anthu onse, Numeri 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Lankhula ndi Aroni ndiponso ana ake kuti, ‘Muzidalitsa+ ana a Isiraeli motere: Yoswa 22:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Atatero, Yoswa anawadalitsa+ n’kuwauza kuti azipita kumahema awo. 1 Mafumu 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako mfumu inatembenuka n’kuyang’ana anthuwo. Ndiyeno inayamba kudalitsa+ mpingo wonse wa Isiraeli. Pamenepo n’kuti mpingo wonse wa Isiraeli utaimirira. 2 Mbiri 30:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pomalizira pake ansembe achilevi anaimirira n’kudalitsa+ anthuwo, ndipo mawu awo anamvedwa moti pemphero lawo linafika kumwamba, kumalo oyera okhala Mulungu.+
23 Pamenepo Mose ndi Aroni analowa m’chihema chokumanako, kenako anatulukamo n’kudalitsa anthuwo.+ Atatero, ulemerero wa Yehova+ unaonekera kwa anthu onse,
14 Kenako mfumu inatembenuka n’kuyang’ana anthuwo. Ndiyeno inayamba kudalitsa+ mpingo wonse wa Isiraeli. Pamenepo n’kuti mpingo wonse wa Isiraeli utaimirira.
27 Pomalizira pake ansembe achilevi anaimirira n’kudalitsa+ anthuwo, ndipo mawu awo anamvedwa moti pemphero lawo linafika kumwamba, kumalo oyera okhala Mulungu.+