Ekisodo 30:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “Upange guwa lansembe la zofukiza.+ Ulipange ndi matabwa a mthethe. Salimo 141:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pemphero langa likhale lokonzedwa ngati zofukiza+ pamaso panu,+Mapembedzero anga akhale ngati nsembe yambewu yamadzulo.+ Luka 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Khamu lonse la anthu linali kupemphera panja, pa ola lopereka nsembe zofukizalo.+ Chivumbulutso 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Atatenga mpukutuwo, zamoyo zinayi ndi akulu 24 aja+ anagwada ndi kuwerama pamaso pa Mwanawankhosa. Aliyense wa iwo anali ndi zeze woimbira+ ndi mbale yagolide yodzaza ndi zofukiza. Zofukizazo+ zikuimira mapemphero+ a oyera.
2 Pemphero langa likhale lokonzedwa ngati zofukiza+ pamaso panu,+Mapembedzero anga akhale ngati nsembe yambewu yamadzulo.+
8 Atatenga mpukutuwo, zamoyo zinayi ndi akulu 24 aja+ anagwada ndi kuwerama pamaso pa Mwanawankhosa. Aliyense wa iwo anali ndi zeze woimbira+ ndi mbale yagolide yodzaza ndi zofukiza. Zofukizazo+ zikuimira mapemphero+ a oyera.